Revelation copertina

Revelation

Revelation

Ascolta gratuitamente

Vedi i dettagli del titolo

Offerte di stagione | 0,99 €/mese per i primi 3 mesi

A seguire 9,99 €/mese – si applicano condizioni. Puoi disdire mensilmente.
0:00 Mau otsogolera 26:14 Mau otsogolera 50:06 Makhalidwe ya Yesu Kristu 1:13:57 Yohane aperekamalonjendi madalitso ku mipingo isanu ndi iwiri 1:32:05 Kuonetsedwa kwa Kristu 1:55:10 Kristu aonetsedwa m thupi la ulemerero 2:19:42 Matanthauzo a zizindikiro ndi mau otsogolera chapter 2 ndi 3 2:43:16 Kalata yopita kumpingo wa Efeso 3:08:25 Chenjezo ndi madalitso 3:31:39 Kalata yopita kumpingo wa Smurna 3:54:36 Kalata yopita kumpingo wa Pergamo 4:16:48 Kalata yopita kumpingo wa Tiyatira 4:40:15 Kalata yopita kumpingo wa Sarde 5:03:09 Kalata yopita kumpingo wa Filadefeya 5:27:29 Kalata yopita kumpingo wa Laodikaya 5:52:37 Chiweruzo pa akristu wofunda 6:16:42 Zomwe tiyenera kuphunzira kuchokera kumipingo isanu ndi iwiri 6:39:40 Mpando wachifumu wa Mulungu 7:06:04 Zamoyo zinayi 7:29:57 Mpingo ukuoneka m Mwamba ndi Kristu 7:53:49 Kumasula chizindikiro (seal) choyamba 8:18:54 Akavalo anayi ofiira 8:43:05 Imfa ndi chizindikiro chachisanu ndi chisanu ndi chimodzi 9:07:09 Zochitika pakati pa chisindikizo cha chisanu ndi chimodzi ndi chisindikizo cha chisanu ndi chiwiri 9:29:36 Kusindikiza anthu wokhulupirika 9:52:43 Anthu wosindikizidwa ndi woomboledwa 10:16:40 Anthu obvala zobvala zoyera 10:40:49 Kumasula chizindikiro cha chisanu ndi chiwiri 11:05:39 Chizindikiro cha malipenga asanu ndi awiri 11:28:40 Zomwe malipenga anayi, aimira 11:51:40 Lipenga la chisanu 12:14:43 Lipenga lachisanu ndi chimodzi 12:37:38 Zochitika pakati pa lipenga lachisanu ndi chimodzi ndi lipenga lachisanu ndi awiri. 13:00:23 Mngelo wamphamvu ndi kabuku kakang ono 13:24:43 Zochitika pakati pa lipenga la chisanu ndi limodzi ndi lipenga lachisanu ndi lachiwiri 13:48:23 Mboni ziwiri 14:12:54 Lipenga la chisanu ndi chiwiri 14:38:01 Chizindikiro cha mkazi 15:02:21 Chizindikiro cha mwana ndi chinjoka 15:27:15 Satana adzagonjetsedwa kotheratu 15:51:04 Zirombo ziwiri zotsiriza 16:14:48 Chirombo cha maonekedwe ndi makhalidwe osiyana-siyana 16:40:04 Chirombo cha chiwiri 17:04:49 Chithunzi cha Mwanawankhosa akuoneka pamodzi ndi anthu 144,000 17:28:31 Kulalikira Uthenga wachipulumutso ndi kulengeza chilango 17:52:18 Kuunika mathero a zochitika zonse 18:16:37 Woyera mtima a m chisautso chachikuru ali Kumwamba 18:39:52 Woyera mtima a m chisautso chachikuru alambira Mulungu. 19:03:01 Mbale zisanu ndi ziwiri za mkwiyo wa Mulungu 19:26:26 Mbale yachisanu ya mkwiyo wa Mulungu ndi nthawi yopanda zochitika 19:52:27 Mbale yachisanu ndi chiwiri ndi mkazi wachigololo 20:18:03 Mkazi ndi chirombo 20:43:39 Kugwa kwa Babulo mundale ndi pamalonda 21:08:48 Moyo wamasautso pansi pano ndi moyo wachisangalalo Kumwamba 21:32:12 Kulambira Yehova 21:56:17 Mkwati ndi mkwatibwi 22:19:00 Kubwera kachiwiri kwa Ambuye Yesu Kristu 22:40:37 Ufumu wa zaka chikwi 23:06:08 Kumasulidwa kwa Satana 23:30:40 Chiweruzo chotsiriza 23:55:02 Moyo wamuyaya 24:19:43 Moyo watsopano 24:44:51 Maonekedwe kapena chithunzi cha Yerusalemu watsopano 25:06:49 Miyala ya maziko 25:28:46 Mulungu wokhala pakati pa anthu ake 25:53:17 Zinthu Zotsiriza
adbl_web_anon_alc_button_suppression_t1
Ancora nessuna recensione