Revelation copertina

Revelation

Revelation

Ascolta gratuitamente

Vedi i dettagli del titolo

Offerte di stagione | 0,99 €/mese per i primi 3 mesi

A seguire 9,99 €/mese – si applicano condizioni. Puoi disdire mensilmente.
0:00 Mau otsogolera 26:27 Mau otsogolera 50:32 Makhalidwe ya Yesu Kristu 1:14:35 Yohane aperekamalonjendi madalitso ku mipingo isanu ndi iwiri 1:32:54 Kuonetsedwa kwa Kristu 1:56:09 Kristu aonetsedwa m thupi la ulemerero 2:20:54 Matanthauzo a zizindikiro ndi mau otsogolera chapter 2 ndi 3 2:44:43 Kalata yopita kumpingo wa Efeso 3:10:06 Chenjezo ndi madalitso 3:33:33 Kalata yopita kumpingo wa Smurna 3:56:39 Kalata yopita kumpingo wa Pergamo 4:19:01 Kalata yopita kumpingo wa Tiyatira 4:42:43 Kalata yopita kumpingo wa Sarde 5:05:53 Kalata yopita kumpingo wa Filadefeya 5:30:24 Kalata yopita kumpingo wa Laodikaya 5:55:47 Chiweruzo pa akristu wofunda 6:20:04 Zomwe tiyenera kuphunzira kuchokera kumipingo isanu ndi iwiri 6:43:14 Mpando wachifumu wa Mulungu 7:09:48 Zamoyo zinayi 7:33:51 Mpingo ukuoneka m Mwamba ndi Kristu 7:57:58 Kumasula chizindikiro (seal) choyamba 8:23:16 Akavalo anayi ofiira 8:47:42 Imfa ndi chizindikiro chachisanu ndi chisanu ndi chimodzi 9:11:59 Zochitika pakati pa chisindikizo cha chisanu ndi chimodzi ndi chisindikizo cha chisanu ndi chiwiri 9:34:35 Kusindikiza anthu wokhulupirika 9:57:53 Anthu wosindikizidwa ndi woomboledwa 10:22:04 Anthu obvala zobvala zoyera 10:46:29 Kumasula chizindikiro cha chisanu ndi chiwiri 11:11:30 Chizindikiro cha malipenga asanu ndi awiri 11:34:45 Zomwe malipenga anayi, aimira 11:57:58 Lipenga la chisanu 12:21:14 Lipenga lachisanu ndi chimodzi 12:44:18 Zochitika pakati pa lipenga lachisanu ndi chimodzi ndi lipenga lachisanu ndi awiri. 13:07:13 Mngelo wamphamvu ndi kabuku kakang ono 13:31:48 Zochitika pakati pa lipenga la chisanu ndi limodzi ndi lipenga lachisanu ndi lachiwiri 13:55:42 Mboni ziwiri 14:20:27 Lipenga la chisanu ndi chiwiri 14:45:47 Chizindikiro cha mkazi 15:10:16 Chizindikiro cha mwana ndi chinjoka 15:35:20 Satana adzagonjetsedwa kotheratu 15:59:24 Zirombo ziwiri zotsiriza 16:23:25 Chirombo cha maonekedwe ndi makhalidwe osiyana-siyana 16:48:52 Chirombo cha chiwiri 17:13:50 Chithunzi cha Mwanawankhosa akuoneka pamodzi ndi anthu 144,000 17:37:45 Kulalikira Uthenga wachipulumutso ndi kulengeza chilango 18:01:44 Kuunika mathero a zochitika zonse 18:26:14 Woyera mtima a m chisautso chachikuru ali Kumwamba 18:49:38 Woyera mtima a m chisautso chachikuru alambira Mulungu. 19:13:01 Mbale zisanu ndi ziwiri za mkwiyo wa Mulungu 19:36:40 Mbale yachisanu ya mkwiyo wa Mulungu ndi nthawi yopanda zochitika 20:02:56 Mbale yachisanu ndi chiwiri ndi mkazi wachigololo 20:28:45 Mkazi ndi chirombo 20:54:29 Kugwa kwa Babulo mundale ndi pamalonda 21:19:49 Moyo wamasautso pansi pano ndi moyo wachisangalalo Kumwamba 21:43:28 Kulambira Yehova 22:07:49 Mkwati ndi mkwatibwi 22:30:44 Kubwera kachiwiri kwa Ambuye Yesu Kristu 22:52:35 Ufumu wa zaka chikwi 23:18:18 Kumasulidwa kwa Satana 23:43:03 Chiweruzo chotsiriza 24:07:35 Moyo wamuyaya 24:32:26 Moyo watsopano 24:57:48 Maonekedwe kapena chithunzi cha Yerusalemu watsopano 25:20:00 Miyala ya maziko 25:42:11 Mulungu wokhala pakati pa anthu ake 26:06:55 Zinthu Zotsiriza
adbl_web_anon_alc_button_suppression_t1
Ancora nessuna recensione